Miyambo 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Yehova anayala maziko a dziko lapansi mwanzeru.+ Anakhazikitsa kumwamba mozindikira.+ Yeremiya 31:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Yehova amene amapereka dzuwa kuti liziwala masana,Amene amaika malamulo oti mwezi ndi nyenyezi ziziwala usiku,Amene amavundula nyanjaKuti mafunde ake achite phokoso,Amene dzina lake ndi Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, wanena kuti:+ Yeremiya 33:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Yehova wanena kuti, ‘Mofanana ndi mmene ndinakhazikitsira pangano langa loti kukhale masana ndi usiku,+ malamulo akumwamba ndi dziko lapansi,+
35 Yehova amene amapereka dzuwa kuti liziwala masana,Amene amaika malamulo oti mwezi ndi nyenyezi ziziwala usiku,Amene amavundula nyanjaKuti mafunde ake achite phokoso,Amene dzina lake ndi Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, wanena kuti:+
25 Yehova wanena kuti, ‘Mofanana ndi mmene ndinakhazikitsira pangano langa loti kukhale masana ndi usiku,+ malamulo akumwamba ndi dziko lapansi,+