Salimo 136:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iye anapanga kumwamba mwaluso,*+Chifukwa chikondi chake chokhulupirika chidzakhalapo mpaka kalekale. Miyambo 3:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Chifukwa chakuti iye amadziwa zinthu, anagawa madzi akuyaNdipo kumwamba kwa mitambo kunagwetsa mame.+
5 Iye anapanga kumwamba mwaluso,*+Chifukwa chikondi chake chokhulupirika chidzakhalapo mpaka kalekale.
20 Chifukwa chakuti iye amadziwa zinthu, anagawa madzi akuyaNdipo kumwamba kwa mitambo kunagwetsa mame.+