Yeremiya 10:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mawu ake akamveka,Madzi akumwamba amachita mkokomo,+Ndipo amachititsa mitambo* kukwera kuchokera kumalekezero a dziko lapansi.+ Iye amachititsa kuti kukamagwa mvula mphezi zizingʼanima,Ndipo amatulutsa mphepo mʼnyumba zake zosungira.+
13 Mawu ake akamveka,Madzi akumwamba amachita mkokomo,+Ndipo amachititsa mitambo* kukwera kuchokera kumalekezero a dziko lapansi.+ Iye amachititsa kuti kukamagwa mvula mphezi zizingʼanima,Ndipo amatulutsa mphepo mʼnyumba zake zosungira.+