Miyambo 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Usatengere zochita za anthu oipa,Ndipo usayende panjira ya anthu oipa.+