Yeremiya 32:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Ndidzawapatsa mtima umodzi+ komanso kuwachititsa kuti aziyenda mʼnjira imodzi kuti azindiopa nthawi zonse. Ndidzachita zimenezi kuti iwo limodzi ndi ana awo zinthu ziziwayendera bwino.+
39 Ndidzawapatsa mtima umodzi+ komanso kuwachititsa kuti aziyenda mʼnjira imodzi kuti azindiopa nthawi zonse. Ndidzachita zimenezi kuti iwo limodzi ndi ana awo zinthu ziziwayendera bwino.+