Salimo 103:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma Yehova adzapitiriza kusonyeza chikondi chake chokhulupirika mpaka kalekaleKwa anthu amene amamuopa,+Ndipo adzapitiriza kusonyeza chilungamo chake kwa ana a ana awo.+
17 Koma Yehova adzapitiriza kusonyeza chikondi chake chokhulupirika mpaka kalekaleKwa anthu amene amamuopa,+Ndipo adzapitiriza kusonyeza chilungamo chake kwa ana a ana awo.+