Salimo 13:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma ine ndakhulupirira chikondi chanu chokhulupirika+Mtima wanga udzasangalala chifukwa cha chipulumutso chanu.+ Salimo 147:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yehova amasangalala ndi anthu amene amamuopa,+Amene amayembekezera chikondi chake chokhulupirika.+
5 Koma ine ndakhulupirira chikondi chanu chokhulupirika+Mtima wanga udzasangalala chifukwa cha chipulumutso chanu.+
11 Yehova amasangalala ndi anthu amene amamuopa,+Amene amayembekezera chikondi chake chokhulupirika.+