Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mbiri 28:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Ndipo iwe Solomo mwana wanga, dziwa Mulungu wa bambo wako ndipo uzimutumikira ndi mtima wonse+ komanso mosangalala, chifukwa Yehova amafufuza mitima yonse+ ndipo amazindikira maganizo a munthu ndi zolinga zake zonse.+ Ukamufunafuna, adzalola kuti umupeze,+ koma ukamusiya iye adzakusiya mpaka kalekale.+

  • 2 Mbiri 15:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Choncho iye anapita kukakumana ndi Asa nʼkumuuza kuti: “Tamverani mfumu Asa ndi anthu onse a fuko la Yuda ndi Benjamini. Yehova akhala nanu inuyo mukapitiriza kukhala naye.+ Mukamufunafuna iye adzalola kuti mumʼpeze,+ koma mukamusiya nayenso adzakusiyani.+

  • 2 Mbiri 19:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Kenako Yehosafati mfumu ya Yuda anabwerera mwamtendere kunyumba kwake*+ ku Yerusalemu.

  • 2 Mbiri 19:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Komabe, pali zinthu zabwino zimene zapezeka mwa inu+ chifukwa mwachotsa mizati yopatulika* mʼdzikoli ndiponso mwakonza mtima wanu kuti mufunefune Mulungu woona.”+

  • Yesaya 55:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Funafunani Yehova pa nthawi imene akupezeka.+

      Muitaneni adakali pafupi.+

  • 1 Petulo 3:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Maso a Yehova* ali pa olungama, ndipo makutu ake amamva mapemphero awo opembedzera,+ koma Yehova* amakwiyira anthu amene amachita zoipa.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena