Salimo 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mudzawononga anthu amene amalankhula mabodza.+ Yehova amadana ndi anthu achiwawa komanso achinyengo.*+ Miyambo 10:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kuopa Yehova kumatalikitsa moyo,+Koma zaka za anthu oipa zidzafupikitsidwa.+
6 Mudzawononga anthu amene amalankhula mabodza.+ Yehova amadana ndi anthu achiwawa komanso achinyengo.*+