Salimo 56:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndimadalira Mulungu, ndimamutamanda chifukwa cha mawu ake.Ine ndimadalira Mulungu, sindikuopa. Kodi munthu wamba angandichite chiyani?+ Yesaya 51:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndimvereni, inu anthu amene mumadziwa chilungamo,Inu anthu amene chilamulo changa chili* mumtima mwanu.+ Musachite mantha ndi mawu otonza amene anthu akunenaNdipo musaope chifukwa cha mawu awo onyoza. Yesaya 51:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Ineyo ndi amene ndikukutonthoza.+ Ndiye nʼchifukwa chiyani ukuopa munthu woti adzafa+Ndiponso mwana wa munthu amene adzanyale ngati udzu wobiriwira?
4 Ndimadalira Mulungu, ndimamutamanda chifukwa cha mawu ake.Ine ndimadalira Mulungu, sindikuopa. Kodi munthu wamba angandichite chiyani?+
7 Ndimvereni, inu anthu amene mumadziwa chilungamo,Inu anthu amene chilamulo changa chili* mumtima mwanu.+ Musachite mantha ndi mawu otonza amene anthu akunenaNdipo musaope chifukwa cha mawu awo onyoza.
12 “Ineyo ndi amene ndikukutonthoza.+ Ndiye nʼchifukwa chiyani ukuopa munthu woti adzafa+Ndiponso mwana wa munthu amene adzanyale ngati udzu wobiriwira?