Salimo 94:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pamene ndinanena kuti: “Phazi langa likuterereka,” Chikondi chanu chokhulupirika, inu Yehova, chinapitiriza kundithandiza.+ Salimo 116:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inu mwandipulumutsa ku imfa,Mwapukuta misozi yanga ndipo mwateteza phazi langa kuti lisapunthwe.+
18 Pamene ndinanena kuti: “Phazi langa likuterereka,” Chikondi chanu chokhulupirika, inu Yehova, chinapitiriza kundithandiza.+