1 Samueli 19:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako Sauli anatumiza anthu kuti akazungulire nyumba ya Davide kuti mʼmawa mwake amuphe.+ Koma Mikala mkazi wa Davide anauza Davideyo kuti: “Ngati suthawa* usiku uno, mawa uphedwa.”
11 Kenako Sauli anatumiza anthu kuti akazungulire nyumba ya Davide kuti mʼmawa mwake amuphe.+ Koma Mikala mkazi wa Davide anauza Davideyo kuti: “Ngati suthawa* usiku uno, mawa uphedwa.”