1 Samueli 19:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kenako Sauli anauza mwana wake Yonatani komanso atumiki ake onse kuti akufuna kupha Davide.+ Salimo 10:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Amadikirira anthu pamalo amene iye amabisala ngati mkango umene uli pamalo ake amene umabisala.*+ Amadikirira kuti agwire munthu wovutika. Amagwira munthu wovutikayo pomukulunga ndi ukonde wake.+ Salimo 71:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Adani anga amandinenera zoipa,Ndipo anthu amene akufuna kuchotsa moyo wanga, amandikonzera chiwembu,+
9 Amadikirira anthu pamalo amene iye amabisala ngati mkango umene uli pamalo ake amene umabisala.*+ Amadikirira kuti agwire munthu wovutika. Amagwira munthu wovutikayo pomukulunga ndi ukonde wake.+
10 Adani anga amandinenera zoipa,Ndipo anthu amene akufuna kuchotsa moyo wanga, amandikonzera chiwembu,+