Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 24:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Bambo anga, onani kansalu aka, kamʼmunsi mwa mkanjo wanu wodula manja. Pamene ndimadula kansalu kameneka sindinakupheni. Ndiye mukhoza kuona kuti ndilibe maganizo oipa kapena oukira, ndipo sindinakuchimwireni.+ Koma inuyo mukufunafuna moyo wanga kuti mundiphe.+

  • 1 Samueli 26:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Davide ananenanso kuti: “Nʼchifukwa chiyani mbuyanga mukundithamangitsa ine mtumiki wanu?+ Ndachita chiyani ine, ndipo ndalakwa chiyani?+

  • Salimo 69:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Anthu amene amadana nane popanda chifukwa+

      Ndi ambiri kuposa tsitsi lamʼmutu mwanga.

      Amene akufuna kuchotsa moyo wanga,

      Adani anga,* omwe ndi anthu achinyengo, achuluka kwambiri.

      Anandikakamiza kuti ndibweze zinthu zimene sindinabe.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena