Salimo 9:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yehova adzakhala malo otetezeka* komwe anthu oponderezedwa angathawireko,+Malo otetezeka othawirako pa nthawi ya mavuto.+ Salimo 62:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye ndi thanthwe langa komanso ndi amene amandipulumutsa, malo anga othawirako otetezeka.*+Sindidzagwedezeka kwambiri.+
9 Yehova adzakhala malo otetezeka* komwe anthu oponderezedwa angathawireko,+Malo otetezeka othawirako pa nthawi ya mavuto.+
2 Iye ndi thanthwe langa komanso ndi amene amandipulumutsa, malo anga othawirako otetezeka.*+Sindidzagwedezeka kwambiri.+