Salimo 109:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Chifukwa anthu oipa ndiponso achinyengo akundinenera zinthu zoipa Iwo akulankhula zinthu zabodza zokhudza ine.+ Salimo 109:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ana ake* aziyendayenda ndipo akhale opemphapempha.Azichoka mʼmabwinja mmene akukhala, nʼkukafunafuna chakudya.
2 Chifukwa anthu oipa ndiponso achinyengo akundinenera zinthu zoipa Iwo akulankhula zinthu zabodza zokhudza ine.+ Salimo 109:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ana ake* aziyendayenda ndipo akhale opemphapempha.Azichoka mʼmabwinja mmene akukhala, nʼkukafunafuna chakudya.
10 Ana ake* aziyendayenda ndipo akhale opemphapempha.Azichoka mʼmabwinja mmene akukhala, nʼkukafunafuna chakudya.