1 Samueli 17:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Davide anawonjezera kuti: “Yehova amene anandipulumutsa mʼkamwa mwa mkango ndi mʼkamwa mwa chimbalangondo andipulumutsanso mʼmanja mwa Mfilisiti ameneyu.”+ Sauli anauza Davide kuti: “Pita, ndipo Yehova akhale nawe.” Salimo 61:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chifukwa inu ndinu malo anga othawirako,Nsanja yolimba imene imanditeteza kwa mdani.+
37 Davide anawonjezera kuti: “Yehova amene anandipulumutsa mʼkamwa mwa mkango ndi mʼkamwa mwa chimbalangondo andipulumutsanso mʼmanja mwa Mfilisiti ameneyu.”+ Sauli anauza Davide kuti: “Pita, ndipo Yehova akhale nawe.”