2 Samueli 10:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tikuyenera kuchita zinthu mwamphamvu komanso molimba mtima+ chifukwa cha anthu athu ndiponso chifukwa cha mizinda ya Mulungu wathu. Yehova adzachita zimene akuona kuti nʼzabwino kwa iye.”+ Salimo 44:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndi mphamvu zanu tidzathamangitsa adani athu.+Mʼdzina lanu tidzagonjetsa anthu amene akutiukira.+
12 Tikuyenera kuchita zinthu mwamphamvu komanso molimba mtima+ chifukwa cha anthu athu ndiponso chifukwa cha mizinda ya Mulungu wathu. Yehova adzachita zimene akuona kuti nʼzabwino kwa iye.”+