Salimo 38:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Anthu amene akufunafuna moyo wanga anditchera misampha,Amene akufuna kundivulaza akukambirana zoti andiwononge,+Tsiku lonse iwo amapanga pulani yoti andinamize.
12 Anthu amene akufunafuna moyo wanga anditchera misampha,Amene akufuna kundivulaza akukambirana zoti andiwononge,+Tsiku lonse iwo amapanga pulani yoti andinamize.