Salimo 16:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndimaika Yehova patsogolo panga nthawi zonse.+ Chifukwa iye ali kudzanja langa lamanja, sindidzagwedezeka.*+ Miyambo 10:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Wolungama sadzagwetsedwa,+Koma anthu oipa sadzakhalanso padziko lapansi.+
8 Ndimaika Yehova patsogolo panga nthawi zonse.+ Chifukwa iye ali kudzanja langa lamanja, sindidzagwedezeka.*+