Salimo 95:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 95 Bwerani, tiyeni tifuule kwa Yehova mosangalala! Tiyeni tifuule mosangalala ndipo titamande Thanthwe la chipulumutso chathu.+ Yesaya 26:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Muzidalira Yehova mpaka kalekale,+Chifukwa Ya,* Yehova ndi Thanthwe lamuyaya.+
95 Bwerani, tiyeni tifuule kwa Yehova mosangalala! Tiyeni tifuule mosangalala ndipo titamande Thanthwe la chipulumutso chathu.+