Salimo 56:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iwo amandibisalira kuti andiukire,Nthawi zonse amaonetsetsa mmene ndikuyendera,+Pofuna kuchotsa moyo wanga.+ Salimo 109:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Chifukwa anthu oipa ndiponso achinyengo akundinenera zinthu zoipa Iwo akulankhula zinthu zabodza zokhudza ine.+
6 Iwo amandibisalira kuti andiukire,Nthawi zonse amaonetsetsa mmene ndikuyendera,+Pofuna kuchotsa moyo wanga.+
2 Chifukwa anthu oipa ndiponso achinyengo akundinenera zinthu zoipa Iwo akulankhula zinthu zabodza zokhudza ine.+