Salimo 12:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehova wanena kuti: “Chifukwa chakuti ovutika akuponderezedwaChifukwa cha kuusa moyo kwa anthu osauka,+Ndidzanyamuka nʼkuchitapo kanthu, Ndidzawapulumutsa kwa anthu amene akuwanyoza.”* Salimo 72:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ateteze* anthu onyozeka pakati pa anthu,Apulumutse ana a anthu osauka,Ndipo aphwanye wobera anzake mwachinyengo.+
5 Yehova wanena kuti: “Chifukwa chakuti ovutika akuponderezedwaChifukwa cha kuusa moyo kwa anthu osauka,+Ndidzanyamuka nʼkuchitapo kanthu, Ndidzawapulumutsa kwa anthu amene akuwanyoza.”*
4 Ateteze* anthu onyozeka pakati pa anthu,Apulumutse ana a anthu osauka,Ndipo aphwanye wobera anzake mwachinyengo.+