Salimo 22:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Anthu onse ochokera kumalekezero a dziko lapansi adzakumbukira Yehova nʼkupita kwa iye. Ndipo mabanja onse a mitundu ya anthu adzagwada pamaso panu.+
27 Anthu onse ochokera kumalekezero a dziko lapansi adzakumbukira Yehova nʼkupita kwa iye. Ndipo mabanja onse a mitundu ya anthu adzagwada pamaso panu.+