Salimo 93:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 93 Yehova wakhala Mfumu!+ Iye wavala ulemerero.Yehova wavala mphamvuWazivala ngati lamba wamʼchiuno. Dziko lapansi lakhazikika,Moti silingasunthidwe.*
93 Yehova wakhala Mfumu!+ Iye wavala ulemerero.Yehova wavala mphamvuWazivala ngati lamba wamʼchiuno. Dziko lapansi lakhazikika,Moti silingasunthidwe.*