Salimo 89:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Nyanja ikadzaza mumailamulira.+Mafunde ake akawinduka, inuyo mumawachititsa kuti akhale bata.+ Salimo 107:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Iye amachititsa kuti mphepo yamkuntho ikhale bata,Mafunde apanyanja amadekha.+