Salimo 147:7, 8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Imbirani Yehova nyimbo moyamikira.Imbirani Mulungu wathu nyimbo zomutamanda pogwiritsa ntchito zeze. 8 Imbirani amene amaphimba mapiri ndi mitambo,Amene amapereka mvula padziko lapansi,+Amenenso amameretsa udzu+ mʼmapiri.
7 Imbirani Yehova nyimbo moyamikira.Imbirani Mulungu wathu nyimbo zomutamanda pogwiritsa ntchito zeze. 8 Imbirani amene amaphimba mapiri ndi mitambo,Amene amapereka mvula padziko lapansi,+Amenenso amameretsa udzu+ mʼmapiri.