Yesaya 37:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Chifukwa kundipsera mtima kwako+ ndi kufuula kwako zafika mʼmakutu mwanga.+ Choncho ndidzakola mphuno yako ndi ngowe yanga ndipo ndidzamanga zingwe zanga+ pakamwa pako.Kenako ndidzakukoka nʼkukubweza kudzera njira imene unadutsa pobwera.”
29 Chifukwa kundipsera mtima kwako+ ndi kufuula kwako zafika mʼmakutu mwanga.+ Choncho ndidzakola mphuno yako ndi ngowe yanga ndipo ndidzamanga zingwe zanga+ pakamwa pako.Kenako ndidzakukoka nʼkukubweza kudzera njira imene unadutsa pobwera.”