1 Samueli 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Amateteza mapazi a okhulupirika ake,+Koma anthu oipa adzawakhalitsa chete mumdima,+Popeza munthu sapambana chifukwa cha mphamvu zake.+ Salimo 121:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iye sadzalola kuti phazi lako literereke.*+ Amene akukuyangʼanira sadzawodzera.
9 Amateteza mapazi a okhulupirika ake,+Koma anthu oipa adzawakhalitsa chete mumdima,+Popeza munthu sapambana chifukwa cha mphamvu zake.+