Yobu 27:8, 9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kodi munthu woipa* akawonongedwa amakhala ndi chiyembekezo chilichonse,+Mulungu akachotsa moyo wake? 9 Kodi Mulungu adzamva kulira kwakeMavuto akadzamugwera?+ Miyambo 15:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Yehova ali kutali ndi anthu oipa,Koma amamva pemphero la anthu olungama.+ Miyambo 28:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Munthu amene amakana kumvera chilamulo,Ngakhale pemphero lake limakhala lonyansa.+ Yesaya 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndipo mukatambasula manja anu,Ndimakubisirani maso anga.+ Ngakhale mupereke mapemphero ambiri,+Ine sindimvetsera.+Manja anu adzaza magazi.+ Yohane 9:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Tikudziwa kuti Mulungu samvetsera ochimwa,+ koma ngati munthu amaopa Mulungu ndipo amachita chifuniro chake, munthu ameneyo amamumvetsera.+
8 Kodi munthu woipa* akawonongedwa amakhala ndi chiyembekezo chilichonse,+Mulungu akachotsa moyo wake? 9 Kodi Mulungu adzamva kulira kwakeMavuto akadzamugwera?+
15 Ndipo mukatambasula manja anu,Ndimakubisirani maso anga.+ Ngakhale mupereke mapemphero ambiri,+Ine sindimvetsera.+Manja anu adzaza magazi.+
31 Tikudziwa kuti Mulungu samvetsera ochimwa,+ koma ngati munthu amaopa Mulungu ndipo amachita chifuniro chake, munthu ameneyo amamumvetsera.+