Numeri 6:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Yehova asonyeze kuti akusangalala nanu+ ndipo akukomereni mtima. Miyambo 16:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mfumu ikamukomera munthu mtima, munthuyo amakhala ndi moyo wabwino.Kukoma mtima kwake kuli ngati mtambo wa mvula mʼnyengo ya chilimwe.+
15 Mfumu ikamukomera munthu mtima, munthuyo amakhala ndi moyo wabwino.Kukoma mtima kwake kuli ngati mtambo wa mvula mʼnyengo ya chilimwe.+