-
Yesaya 49:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Yehova wanena kuti:
“Pa nthawi yosonyeza kukoma mtima kwanga, ndinakuyankha.+
Ndipo pa tsiku la chipulumutso ndinakuthandiza.+
Ndinkakuteteza kuti ndikupereke ngati pangano kwa anthu,+
Kuti ndikonzenso dzikolo,
Kuti anthuwo atengenso cholowa chawo chimene chinali bwinja,+
-