Salimo 69:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndamira mʼmatope akuya, mmene mulibe malo oponda.+ Ndalowa mʼmadzi akuya,Ndipo mtsinje wa madzi othamanga wandikokolola.+
2 Ndamira mʼmatope akuya, mmene mulibe malo oponda.+ Ndalowa mʼmadzi akuya,Ndipo mtsinje wa madzi othamanga wandikokolola.+