Salimo 31:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndikomereni mtima inu Yehova, chifukwa ndavutika kwambiri. Maso anga afooka chifukwa cha chisoni,+ chimodzimodzinso thupi langa lonse.*+ Salimo 40:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mukhale wofunitsitsa kundipulumutsa, inu Yehova.+ Ndithandizeni mofulumira, inu Yehova.+
9 Ndikomereni mtima inu Yehova, chifukwa ndavutika kwambiri. Maso anga afooka chifukwa cha chisoni,+ chimodzimodzinso thupi langa lonse.*+