Salimo 21:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mudzawawononga ngati kuti mwawaponya mungʼanjo yamoto, pa nthawi imene mudzaonekere. Yehova adzawameza atakwiya ndipo moto udzawapsereza.+
9 Mudzawawononga ngati kuti mwawaponya mungʼanjo yamoto, pa nthawi imene mudzaonekere. Yehova adzawameza atakwiya ndipo moto udzawapsereza.+