Yesaya 61:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ana awo* adzadziwika pakati pa mitundu ya anthu,+Ndipo mbadwa zawo zidzadziwika pakati pa anthu osiyanasiyana. Anthu onse owaona adzawazindikira,Kuti ndi ana amene* Yehova anawadalitsa.”+ Yesaya 66:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Chifukwa kumwamba kwatsopano ndi dziko lapansi latsopano+ zimene ndikupanga zidzapitiriza kukhala pamaso panga. Mofanana ndi zimenezi, ana anu* ndi dzina lanu zidzapitiriza kukhalapo,”+ akutero Yehova.
9 Ana awo* adzadziwika pakati pa mitundu ya anthu,+Ndipo mbadwa zawo zidzadziwika pakati pa anthu osiyanasiyana. Anthu onse owaona adzawazindikira,Kuti ndi ana amene* Yehova anawadalitsa.”+
22 “Chifukwa kumwamba kwatsopano ndi dziko lapansi latsopano+ zimene ndikupanga zidzapitiriza kukhala pamaso panga. Mofanana ndi zimenezi, ana anu* ndi dzina lanu zidzapitiriza kukhalapo,”+ akutero Yehova.