1 Mafumu 4:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ayuda ndi Aisiraeli anachuluka kwambiri ngati mchenga wa mʼmbali mwa nyanja+ ndipo ankadya, kumwa komanso kusangalala.+
20 Ayuda ndi Aisiraeli anachuluka kwambiri ngati mchenga wa mʼmbali mwa nyanja+ ndipo ankadya, kumwa komanso kusangalala.+