Numeri 14:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Komanso, pali ine Mulungu wamoyo, dziko lonse lapansi lidzadzaza ndi ulemerero wa Yehova.+ Habakuku 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Chifukwa dziko lapansi lidzadzaza ndi anthu odziwa ulemerero wa Yehova,Ngati mmene madzi amadzazira nyanja.+
14 Chifukwa dziko lapansi lidzadzaza ndi anthu odziwa ulemerero wa Yehova,Ngati mmene madzi amadzazira nyanja.+