1 Samueli 17:58 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 58 Ndiyeno Sauli anamufunsa kuti: “Mnyamata iwe, kodi bambo ako ndi ndani?” Davide anayankha kuti: “Ndine mwana wa mtumiki wanu Jese,+ wa ku Betelehemu.”+
58 Ndiyeno Sauli anamufunsa kuti: “Mnyamata iwe, kodi bambo ako ndi ndani?” Davide anayankha kuti: “Ndine mwana wa mtumiki wanu Jese,+ wa ku Betelehemu.”+