Salimo 37:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Ine ndaona munthu wankhanza komanso woipaZinthu zikumuyendera bwino ngati mtengo wa masamba obiriwira bwino panthaka yake.+
35 Ine ndaona munthu wankhanza komanso woipaZinthu zikumuyendera bwino ngati mtengo wa masamba obiriwira bwino panthaka yake.+