Yobu 7:17, 18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kodi munthu ndi ndani kuti muzida naye nkhawa,Nʼkumamuganizira?*+ 18 Nʼchifukwa chiyani mumamuyendera mʼmawa uliwonse,Nʼkumamuyesa nthawi zonse?+
17 Kodi munthu ndi ndani kuti muzida naye nkhawa,Nʼkumamuganizira?*+ 18 Nʼchifukwa chiyani mumamuyendera mʼmawa uliwonse,Nʼkumamuyesa nthawi zonse?+