Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 42:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Mofanana ndi munthu amene akulakalaka madzi, ndikulakalaka* Mulungu, Mulungu wamoyo.+

      Ndidzapita liti kukaonekera pamaso pa Mulungu?*+

  • Salimo 84:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Moyo wanga ukulakalaka kwambiri,

      Inde, ndafookeratu chifukwa cholakalaka

      Mabwalo a Yehova.+

      Mtima wanga ndi thupi langa zikufuula mosangalala kwa Mulungu wamoyo.

  • Yesaya 26:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Usiku ndimakulakalakani ndi mtima wanga wonse,

      Inde, ndimakufunafunani ndi mtima wonse.+

      Chifukwa mukaweruza dziko lapansi,

      Anthu okhala mʼdzikoli amaphunzira zokhudza chilungamo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena