Salimo 16:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehova ndi gawo langa, gawo limene ndinapatsidwa+ komanso kapu yanga.+ Inu mumateteza cholowa changa. Maliro 3:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ine ndanena kuti: “Yehova ndi cholowa changa.+ Pa chifukwa chimenechi, ndidzakhala ndi mtima womudikira.”+
5 Yehova ndi gawo langa, gawo limene ndinapatsidwa+ komanso kapu yanga.+ Inu mumateteza cholowa changa.
24 Ine ndanena kuti: “Yehova ndi cholowa changa.+ Pa chifukwa chimenechi, ndidzakhala ndi mtima womudikira.”+