Yesaya 48:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Iwo sanamve ludzu pamene iye ankawatsogolera kudutsa mʼchipululu.+ Iye anachititsa kuti madzi atuluke pathanthwe kuti iwo amwe.Anangʼamba thanthwe nʼkupangitsa kuti madzi atuluke.”+
21 Iwo sanamve ludzu pamene iye ankawatsogolera kudutsa mʼchipululu.+ Iye anachititsa kuti madzi atuluke pathanthwe kuti iwo amwe.Anangʼamba thanthwe nʼkupangitsa kuti madzi atuluke.”+