Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 89:50, 51
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 50 Inu Yehova, kumbukirani mmene atumiki anu anyozedwera.

      Kumbukirani mmene ndapiririra* kunyozedwa kochokera ku mitundu yonse ya anthu.

      51 Inu Yehova, kumbukirani mmene adani anu alankhulira monyoza.

      Mmene anyozera paliponse pamene mapazi a wodzozedwa wanu aponda.

  • Yesaya 52:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Tsopano kodi nditani pamenepa?” akutero Yehova.

      “Chifukwa anthu anga anatengedwa kwaulere.

      Amene ankawalamulira ankangokhalira kufuula posonyeza kuti apambana.+

      Tsiku lililonse ndinkaona kuti dzina langa silikulemekezedwa,”+ akutero Yehova.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena