Yesaya 30:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Taonani! Dzina la Yehova likubwera kuchokera kutali.Likubwera ndi mkwiyo wake woyaka moto ndiponso mitambo yolemera. Iye akulankhula mwaukali,Ndipo lilime lake lili ngati moto wowononga.+
27 Taonani! Dzina la Yehova likubwera kuchokera kutali.Likubwera ndi mkwiyo wake woyaka moto ndiponso mitambo yolemera. Iye akulankhula mwaukali,Ndipo lilime lake lili ngati moto wowononga.+