Deuteronomo 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma samalani ndipo mukhale tcheru* kuti musaiwale zinthu zimene maso anu anaona, komanso kuti zinthu zimenezo zisachoke mumtima mwanu masiku onse a moyo wanu. Ana anu ndi zidzukulu zanu muziwauzanso zinthu zimenezo.+ Salimo 103:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Moyo wanga utamande Yehova,Ndisaiwale zinthu zonse zimene wachita.+
9 Koma samalani ndipo mukhale tcheru* kuti musaiwale zinthu zimene maso anu anaona, komanso kuti zinthu zimenezo zisachoke mumtima mwanu masiku onse a moyo wanu. Ana anu ndi zidzukulu zanu muziwauzanso zinthu zimenezo.+