Salimo 106:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iwo anasonyeza mtima wadyera mʼchipululu,+Ndipo anayesa Mulungu mʼchipululumo.+