-
Aheberi 3:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Nʼchifukwa chake ndinanyansidwa ndi mʼbadwo umenewo, ndipo ndinati, ‘Mitima yawo imasochera nthawi zonse ndipo njira zanga sakuzidziwa.’
-