Numeri 14:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Komabe anthu onse amene aona ulemerero wanga ndi zizindikiro zanga+ zimene ndinachita ku Iguputo, komanso zimene ndachita mʼchipululu, koma apitiriza kundiyesa+ maulendo 10 onsewa, ndipo sanamvere mawu anga,+ Deuteronomo 6:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Yehova Mulungu wanu musamamuyese+ ngati mmene munamuyesera ku Masa.+ Salimo 95:8, 9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Musaumitse mitima yanu ngati mmene makolo anu anachitira ku Meriba,*+Ngati mmene anachitira ku Masa* mʼchipululu,+ 9 Pamene makolo anu anandiyesa.+Iwo anatsutsana ndi ine ngakhale kuti anaona ntchito zanga.+
22 Komabe anthu onse amene aona ulemerero wanga ndi zizindikiro zanga+ zimene ndinachita ku Iguputo, komanso zimene ndachita mʼchipululu, koma apitiriza kundiyesa+ maulendo 10 onsewa, ndipo sanamvere mawu anga,+
8 Musaumitse mitima yanu ngati mmene makolo anu anachitira ku Meriba,*+Ngati mmene anachitira ku Masa* mʼchipululu,+ 9 Pamene makolo anu anandiyesa.+Iwo anatsutsana ndi ine ngakhale kuti anaona ntchito zanga.+